CHIKONDI LYRICS Verse 1 Mukandiwona ine ndilinkulakwitsa (If you see me in error) Mundikonze mwa chikondi (Correct me with love) Kusiyana ndikuti mukawuze wina (Instead of going to tell someone else) Mundiphela chikoka changa (You will kill my influence) Tikamuwona mbale, mlongo, alinkulakwitsa (If we see a brother, sister, in error) Timukonze mwa chikondi (Let’s […]